Track
Zed-Pop
Oh yeah it's Driemo Mbendera peru Peru Nthungululu Unadumpha mtima wanga utangovomera Ndinagwidwa tsembwe Ndinawumaa I couldn't feel my legs utangoyankhula Oh oh Zapamwambaaa Zapamwambaaaaa Oh yeah Sing again Zapamwambaaa Zapamwambaaa Uh yeah uh yeah Ndizakukonda Konda konda Babe sizamwana Sizamwana Nawenso udzandikonda Konda konda Babe sizamwana Sizamwana Do you how it feels When I think of you Ooooh yeah Umandisintha level level Undilemekeza babe I can't thank you enough Zapamwamba Zapamwambaaaa Oooh yeah Zachikondizi Zapamwambaaa Zapamwambaaa Ndizakukonda Konda konda Babe sizamwana Sizamwana Nawenso udzandikonda Konda konda Babe sizamwana Sizamwana Konda Kooondaaa Sizaaamwaaanaaa
Follow our WhatsApp Channel
Get the latest Zambian music updates
Sign in to leave a comment